Lyrisc: Onesimus – Panado (translated)

Onesimus - Panado

Lyrisc: Onesimus – Panado (translated)

INTRO
Panado Panado yeah Mmm ma headache yeah Mmm eeh
Panado Panado mmm eeh
VERSE1
Amakonda miseche (They love gossiping)
Amakondwa munthu adzivutika (They’re happy when others suffer)
Zochitika ngati siopemphera (They behave like non-believers)
Daily daily busy ntopola
(Their daily lifestyle full of squabbles)
Kubaya ma damage (Injuring reputations)
Kuupasa moyo wanga challenge (Giving my life a challenge)
Machitidwe awo ngati Judas (Their deeds are like Judas)
Makhalidwe awo ngati njenjete eeh (They behave like fleas)

PRE-CHORUS
Amafuna ndikokoloke
(They want me washed away)
Amakhumbira nditaphokoloka (They just wish I tumbled)
Amafuna ndisokoloke (They want me gone)
Amafuna mwina nditakomoka (Or wish I was in a coma)

Amafuna ndikokoloke
(They want me washed away)
Amakhumbira nditaphokoloka (They just wish I tumbled)
Amafuna ndisokoloke (They want me gone)
Amafuna mwina nditakomoka (Or wish I was in a coma)

CHORUS
Ndi nsanje apatseni, Panado Panado (It’s jealousy give them, Panado Panado)
Panado Panado
Amweko Panado Panado (Let them take Panado)
Panado Panado (yeah yeah)
Mutu wakula ndi nsanje (Heavy-headed because of jealousy)
Kaduka ndi nsanje (Envy and jealousy
Kaduka mwina ndi nsanje (Perhaps it’s envy and jealousy)
Kaduka, mtima wachigawega (Envy, life of a dissident)
Mutu wakula ndi nsanje (Heavy-headed because of jealousy)
Kaduka ndi nsanje (Envy and jealousy
Kaduka ndi nsanje
(Perhaps it’s envy and jealousy)
Kaduka, mtima wachigawega (Envy, life of a dissident)

VERSE 2
Samafuna ndiyendere njale (They don’t want me driving)
Samakondwa ndikamadya money
(Not happy when I’m living life to the fullest)
Zikandiyendera amakoka chibale
(When times are good they want us close)
Zikamandivuta andinyoza kumbali (They back bite me when it’s not rosy)
Koma Mulungu andichita balance, I relax (But God balances me, I relax)
Amamenya nkhondo nditakhala pansi (He fights for me while I’m laid-back)
Adani anga onse alemba m’madzi (All my enemies will despair)
Samakondwa nane (They’re not happy with me)

PRE-CHORUS
Amafuna ndikokoloke
(They want me washed away)
Amakhumbira nditaphokoloka (They just wish I tumbled)
Amafuna ndisokoloke (They want me gone)
Amafuna mwina nditakomoka (Or wish I was in a coma)
Amafuna ndikokoloke
(They want me washed away)
Amakhumbira nditaphokoloka (They just wish I tumbled)
Amafuna ndisokoloke (They want me gone)
Amafuna mwina nditakomoka (Or wish I was in a coma)

CHORUS
Ndi nsanje apatseni, Panado Panado (It’s jealousy give them, Panado Panado)
Panado Panado
Amweko Panado Panado (Let them take Panado)
Panado Panado (yeah yeah)
Mutu wakula ndi nsanje (Heavy-headed because of jealousy)
Kaduka ndi nsanje (Envy and jealousy
Kaduka mwina ndi nsanje (Perhaps it’s envy and jealousy)
Kaduka, mtima wachigawega (Envy, life of a dissident)
Mutu wakula ndi nsanje (Heavy-headed because of jealousy)
Kaduka ndi nsanje (Envy and jealousy
Kaduka ndi nsanje
(Perhaps it’s envy and jealousy)
Kaduka, mtima wachigawega (Envy, life of a dissident).

Similar Posts:

Author: Admin Boss

Leave a Reply

Your email address will not be published.